É o King Chex Haaaaa, the only, the only Ndiwe wekha, iwe wekha, ndiwe wanga Ndiwe wanga, beby yanga, nkazi wanga Baby ine ndimakonda iwe wekha Baby ine ndimafuna iwe wekha Love yanga ndimapatsa iwe wekha Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga Ndiwe wekha unatenga Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love) (My love) (My love) Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love) (My love) (My love) Padziko assanje alipo ambiri Tiye tikondane m'mene tililj Iwe ndi ine tipangue mbiri, (huuuu mbiri) Opanda iwe sinditha kukhala Opanda iwe baby ine ndimamala Zokamba kamba ossawavela Kukhala ndiwe, baby ine ndimamala Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love) (My love) (My love) Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love) (My love) (My love)